Mawu a M'munsi
c Mboni za Yehova zapeza kuti buku lofotokoza za m’Baibulo lakuti Mafunso Achichepere Akufunsa—Mayankho Amene Amathandiza n’lothandiza kwambiri. Mutu uliwonse mwa mitu yake 39 umayankha funso lochititsa chidwi. Nayi mitu yake ina: “Kodi Ndingapange Bwanji Mabwenzi Enieni?” “Kodi Ndingalake Motani Chitsenderezo cha Ausinkhu Wanga?” “Kodi Ndingachititse Motani Kusukidwa Kwanga Kuchoka?” “Kodi Ndili Wokonzekera Kupalana Ubwenzi?” “Kodi Nkuneneranji Kuti Ayi ku Mankhwala Oledzeretsa?” “Bwanji Ponena za Kugonana Ukwati Usanachitike?”