Mawu a M'munsi
a Mboni za Yehova sizichita nawo zionetsero kapena makampeni a ndale alionse ofuna kusintha malamulo a mādziko mwawo, ngakhale malamulowo akhale osemphana ndi zimene chikumbumtima chawo chimawauza chifukwa choti aphunzira Baibulo.