Mawu a M'munsi
b Kuwonjezera apo, njira imene amaperekera zizindikiro za mafilimu ikhoza kukhala yosiyana m’mayiko osiyanasiyana. Filimu imene aipatsa chizindikiro choti siyoyenera achinyamata m’dziko lina ikhoza kupatsidwa chizindikiro choti ndi yowayenera m’dziko lina.