Mawu a M'munsi
a Mphamvu ya dzuwa ingawonongenso maselo enaake okhala m’kati mwa khungu, amene amathandiza thupi kulimbana ndi matenda. Buku lakuti The Skin Cancer Answer limati: “Chifukwa cha zimenezi asayansi ena akukhulupirira kuti kufooka kwa mphamvu ya thupi lathu yotiteteza ku matenda kumayambitsa khansa yapakhungu.”