Mawu a M'munsi
a Ochita kafukufuku ena amanena kuti “pafupifupi anthu 90 pa 100 alionse a zaka zoposa 65 sadwala matenda a maganizo.” Kuti mumve zambiri zokhudza chithandizo cha matenda a maganizo, onani nkhani zokamba za matenda a Alzheimer’s mu Galamukani! ya October 8, 1998.