Mawu a M'munsi
b Galamukani! silangiza anthu kuti atsatire njira yakutiyakuti ya chithandizo. Akristu ayenera kuonetsetsa kuti chithandizo chilichonse chimene akulandira sichikutsutsana ndi mfundo za m’Baibulo. Onani nkhani zakuti “Kumvetsetsa Matenda a Maganizo,” mu Galamukani! ya January 8, 2004.