Mawu a M'munsi
b Kuchita chigololo kumatanthauza kuchita zinthu monga kugonana kwenikweni, kugonana m’kamwa, kumatako, kugonana amuna kapena akazi okhaokha, kuseweretsa maliseche munthu wina, ndiponso kuchita zinthu zina zokhudzana ndi maliseche, zochitidwa ndi anthu amene sanakwatirane.