Mawu a M'munsi c Kuti njuchi zipange uchi wokwana kilogalamu imodzi yokha, zimafunika kuyenda maulendo 10 miliyoni opita ku maluwa.