Mawu a M'munsi
a Dera limeneli linali la dziko la Spanish Netherlands limene linkalamulidwa ndi dziko la Spain m’zaka za m’ma 1500. Derali linaphatikizapo zigawo zakunyanja za kumpoto kwa France, Belgium, ndi Holland.