Mawu a M'munsi
c Pa zinthu zimene ofesiyi inatchula tasinthako pang’ono zina ndi zina. Malinga ndi dera limene mukukhala, mwina simungafunike kutenga zinthu zonse zimene zalembedwazi, ndipo mwinanso mungawonjezerepo zina. Mwachitsanzo, anthu achikulire ndi olumala ali ndi zinthu zawo zimene amafunikira.