Mawu a M'munsi
b Mpukutuwu unalembedwa kuti upite kwa munthu wina wotchedwa Juliana Anicia, yemwe mwina anamwalira mu 527 C.E. kapena mu 528 C.E. Mpukutuwu “ndi chitsanzo cha mpukutu wakale kwambiri wachikopa wokhala ndi zilembo zikuluzikulu womwe ukudziwika deti lake.”—An Introduction to Greek and Latin Palaeography, lolembedwa ndi E. M. Thompson.