Mawu a M'munsi
c Mabuku amene amatchedwa kuti mabuku a Eusebius kwenikweni ndi mabuku okhala ndi mabokosi ofotokozera malemba, omwe cholinga chake “n’kusonyeza munthu mbali za mabuku a Uthenga Wabwino zomwe zili zofanana.”—Manuscripts of the Greek Bible, lolembedwa ndi Bruce M. Metzger.