Mawu a M'munsi
b Anyaniwa ndi ofanana ndi anyani ena a ku Japan, omwe m’nyengo yozizira amakonda kusonkhana kumene kuli akasupe amadzi otentha. Anthu okaona akasupewa ku Japan amachita chidwi kwambiri ndi anyaniwa.