Mawu a M'munsi
a Yesu ananena chifukwa chimodzi chokha chimene banja lingathere, winayo n’kukwatiranso kapena kukwatiwanso. Iye anati banja lingathe ngati mmodzi wachita chigololo, kutanthauza kugonana ndi munthu wina yemwe si mkazi kapena mwamuna wake.—Mateyo 19:9.