Mawu a M'munsi
c Ngati wina wachita chigololo, Baibulo limalola mnzakeyo kusankha zochita. Iye angasankhe kusudzula wosakhulupirikayo kapena kumukhululukira. (Mateyo 19:9) Onani nkhani yakuti “Lingaliro la Baibulo: Chigololo—Kukhululukira Kapena Kusakhululukira?” mu Galamukani! ya August 8, 1995.