Mawu a M'munsi
b Bungwe la National Aeronautics and Space Administration (NASA) ndi lomwe linatumiza chombo cha Mars Odyssey ndi cha Mars Reconnaissance Orbiter. Ndipo chombo cha Mars Express chinatumizidwa ndi bungwe la European Space Agency.