Mawu a M'munsi
b Mfundozi zachokera ku bungwe la pa dziko lonse loona za matenda olepheretsa kuphunzira (lotchedwa International Dyslexia Association). Onaninso nkhani yakuti “Kuthandiza Ana Amene Ali ndi Vuto Lophunzira” mu Galamukani! ya January 2009.