Mawu a M'munsi
a Baibulo la Dziko la Tsopano pa Yeremiya 39:3, pali mawu akuti, “Samugari-nebo, Sarisekimu, Rabisarisi,” ndipo linatsatira malemba a Chiheberi olembedwa ndi Amasorete. Koma akanatsatira kalembedwe ka Chiheberi, mawuwa akanalembedwa kuti, “Samugari, Nebo-sarisekimu m’Rabusarisi [kapena kuti Mkulu wa Adindo],” ndipo zimenezi zimagwirizana ndi mawu olembedwa m’mapale.