Mawu a M'munsi
a Ngati anthu amene akukhudzidwa aona kuti mayi pobereka, iyeyo kapena mwana wake afa, angasankhe kuti achita bwanji. Komabe zimenezi sizichitikachitika masiku ano, chifukwa mâmayiko ambiri njira zachipatala zapita patsogolo kwambiri.