Mawu a M'munsi
c Si bwino kuganiza kuti muyenera kulira n’cholinga chosonyeza kuti muli ndi chisoni. Dziwani kuti anthu amasonyeza chisoni mosiyanasiyana. Mfundo yofunika ndi yakuti: Mukaona kuti m’maso mwayamba misozi, mwina imeneyo ingakhale “mphindi yakulira.”—Mlaliki 3:4.