Mawu a M'munsi
b Asayansi anatulukira mphamvu imeneyi m’zaka za m’ma 1930 ndipo anazitsimikizira kuti ilipodi m’zaka za m’ma 1980. Masiku ano asayansi amatha kudziwa kuchuluka kwa mphamvu imeneyi mu milalang’amba poona mmene milalang’ambayo imakhotetsera kuwala kochokera ku nyenyezi zakutali kwambiri.