Mawu a M'munsi
c Chaka cha 2009 ndi chaka chokumbukira sayansi ya zinthu zakuthambo ndiponso chokondwerera kuti papita zaka 400 kuchokera pamene Galileo Galilei, anapanga chipangizo choonera zinthu zakuthambo. Mutu wa chaka chino ndi wakuti “Fufuzani Zinthu Zakuthambo.”