Mawu a M'munsi
b Nkhalango imeneyi inayamba kutetezedwa mu 1979 ndipo poyamba inkadziwika ndi dzina lakuti Huanchaca. Nkhalangoyi anaipatsa dzina latsopano mu 1988 pokumbukira wasayansi wina wa ku Bolivia dzina lake Noel Kempff Mercado. Wasayansiyu anaphedwa mânkhalangoyi ndi anthu ozembetsa mankhwala osokoneza bongo, iye atatulukira mwangozi malo amene anthuwa ankakonzera mankhwalawa.