Mawu a M'munsi
b Koma ngati makolo anu sakukukhulupiriranibe, auzeni modekha ndiponso mwaulemu mmene mukumvera. Mvetserani madandaulo awo, ndipo onetsetsani kuti palibe chilichonse chimene mukuchita chomwe chingachititse kuti azikukaikirani.—Yakobe 1:19.