Mawu a M'munsi
a Mawu akuti “dama” samangonena za kugonana basi. Amatanthauzanso zinthu zina zimene anthu osakwatirana angachite, monga kugwiranagwirana maliseche ndiponso kugonana mkamwa kapena kumatako. Mukafune kudziwa zambiri, onani buku lakuti Mayankho a Zimene Achinyamata Amafunsa, Buku Lachiwiri, masamba 42-47.