Mawu a M'munsi
b Pali zinthu zambirimbiri zimene akatswiri akuganiza kuti zimayambitsa chibwibwi ndiponso kuchepetsa vutoli. Nthawi zina akatswiriwa amanena zogwirizana koma nthawi zinanso zonena zawo zimatsutsana. Galamukani! sisankhira anthu thandizo la mankhwala.