Mawu a M'munsi
a Tikudziwa kuti anthu ambiri ali ndi matenda kapena zilema zimene palibe chilichonse chimene angachite kuti asakhale nazo. Nkhani ino ingathandize anthu amenewa kuti akhale ndi thanzi labwinoko ngakhale kuti ali ndi mavuto amenewa.