Mawu a M'munsi
b Mawu akuti dama malinga ndi mmene amagwiritsidwira ntchito m’Baibulo, samangotanthauza kugonana kwa pakati pa mkazi ndi mwamuna amene sanakwatirane. Mawuwa amatanthauzanso kuseweretsana maliseche komanso kugonana m’kamwa kapena kumbuyo.