Mawu a M'munsi
b Ngakhale kuti kumwa mowa kungachititse kuti muiwaleko imfa ya munthu amene mumam’konda, dziwani kuti mowa ndi wosathandiza kwenikweni. Mowa umangokuthandizani kuiwala kwa nthawi yochepa koma m’kupita kwa nthawi, sungakuthandizeninso ndipo mukhoza kukhala ndi chizolowezi chodalira mowa.