Mawu a M'munsi d Kuti mudziwe zambiri zokhudza zimene zimachitika munthu akamwalira komanso lonjezo la Mulungu lakuti akufa adzauka, onani mutu 6 ndi 7 m’buku lakuti Kodi Baibulo Limaphunzitsa Chiyani Kwenikweni? lofalitsidwa ndi Mboni za Yehova.