Mawu a M'munsi
a Lemba la Chivumbulutso 5:11 limanena za angelo “miyanda kuchulukitsa ndi miyanda” amene azungulira mpando wachifumu wa Mulungu. Mwanda umodzi ndi 10,000. Ndiye 10,000 kuchulukitsa ndi 10,000 zimapanga 100 miliyoni. Koma onani kuti lembali likugwiritsa ntchito mawu akuti “miyanda kuchulukitsa ndi miyanda,” kusonyeza kuti chiwerengerochi chikhoza kukhala chachikulu kuposa 100 miliyoni.