Mawu a M'munsi
a Magazini ya Galamukani! siiletsa kapena kulimbikitsa anthu kugwiritsa ntchito malo ena ake ochezera a pa Intaneti. Mkhristu aliyense ayenera kuonetsetsa kuti sakuphwanya malamulo a Mulungu pamene akugwiritsa ntchito malo ochezera a pa Intaneti.—1 Timoteyo 1:5, 19.