Mawu a M'munsi
a M’zilankhulo zoyambirira zimene anagwiritsa ntchito polemba Baibulo, makamaka Chiheberi ndi Chigiriki, dzinali limapezeka nthawi pafupifupi 7,000. Koma n’zomvetsa chisoni kuti Mabaibulo ambiri masiku ano anachotsamo dzina lakuti Yehova n’kuikamo mayina ake audindo.