Mawu a M'munsi
a Tikamaona zinthu zimene zili kutali m’mlengalenga pogwiritsa ntchito makamera oonera kuthambo, mphamvu za maso athu zothandiza kuti tizisiyanitsa mitundu sizigwira ntchito. Mphamvu zimene zimagwira ntchito ndi zimene zimagwira ntchito usiku wokha basi.
[Zithunzi]
Chithunzi cha mitundu iwiri
Chofiira
Chagilini
Chabuluu
Mmene chithunzi chimaonekera akaphatikiza mitundu itatuyi
[Mawu a Chithunzi]
J. Hester and P. Scowen (AZ State Univ.), NASA