Mawu a M'munsi
a Kabuku kena konena za kupsa mtima kamafotokoza kuti munthu amene amapsa mtima mosadziletsa amakumana ndi mavuto ambiri pamoyo wake ndipo zimenezi zimachititsa kuti azilephera kuganiza bwino, azingokhala wokhumudwa komanso asamakhale mwamtendere ndi anthu ena.—Boiling Point—Problem Anger and What We Can Do About It.