Mawu a M'munsi
a Anthu amene amachita uchigawenga wa pa Intaneti amasokoneza kapena kuwononga mwadala makompyuta a anthu ena omwe alumikizidwa pa Intaneti. Zigawengazi zimawononga zinthu zofunikira zokhudza mwini kompyutayo kapena mapulogalamu a pa kompyutayo.—U.S. National Research Council.