Mawu a M'munsi
b Akuti mu 2011, anthu akuba pa Intaneti ankadziwa mavuto oposa 45,000 okhudza makompyuta, ndipo zimenezi zikanawathandiza kuba mosavuta. Chifukwa chodziwa mavuto amenewa, nthawi zambiri mbava zimatumiza pulogalamu yachinyengo yobera kapena kuwononga zinthu m’makopyuta a anthu, eniake asakudziwa.