Mawu a M'munsi
a Kuti mudziwe zambiri pa nkhani imeneyi, werengani nkhani yakuti “Kuthandiza Mwana Wanu Panthawi Yachisoni,” mu Nsanja ya Olonda ya July 1, 2008, patsamba 18 mpaka 20, komanso kabuku kakuti, Pamene Munthu Amene Mumakonda Amwalira, kofalitsidwa ndi Mboni za Yehova.