Mawu a M'munsi
a Ngakhale kuti Plato ndi amene anatchukitsa chiphunzitso chimenechi, sikuti iye ndi amene anachiyambitsa. Zipembedzo zambiri zachikunja zakhala zikukhulupirira chiphunzitso chimenechi m’njira zosiyanasiyana. Zina mwa zipembedzo zimenezi ndi za ku Iguputo ndi Babulo.