Mawu a M'munsi
b Mfundo imeneyi ndi yothandizanso ngati banja linatha. Kaya anawo akukhala ndi bamboyo kapena mayi, ngati bamboyo amalemekezabe mayiyo, zingathandize kuti anawo azilemekezanso mayi awo.