Mawu a M'munsi
b Anthu ambiri amagwiriridwa ndi achibale kapena anthu ena owadziwa. Kuti mudziwe zambiri, onani mutu wakuti, “How Can I Protect Myself From Sexual Predators?” m’buku lachingerezi lakuti Questions Young People Ask—Answers That Work, Volume 1, patsamba 228. Bukuli mukhoza kulipezanso pa Webusaiti yathu www.jw.org.