Mawu a M'munsi
a Zinthu zolaula zimene anthu amatumizirana pafoni zimatha kukhala mameseji, zithunzi kapena mavidiyo. Kuti mudziwe zambiri, pitani pa webusaiti ya jw.org kuti muwerenge nkhani yakuti “Zimene Achinyamata Amadzifunsa—Zimene Ndiyenera Kudziwa Zokhudza Kutumizirana Zinthu Zolaula.”—Fufuzani pa mawu akuti ZIMENE BAIBULO LIMAPHUNZITSA > ACHINYAMATA.