Mawu a M'munsi
a Kuti mudziwe zambiri, pitani pa webusaiti yathu ya jw.org/ny. Pitani pamene palembedwa kuti ZIMENE BAIBULO LIMAPHUNZITSA > ANTHU APABANJA NDIPONSO MAKOLO. Pamenepa mungapezepo nkhani monga yakuti, “Zimene Mungachite Mwana Akayamba Kuvuta” ndi yakuti, “Zimene Mungachite Kuti Mwana Wanu Azikumverani.”