Mawu a M'munsi
a Mulungu ali ndi thupi ngati la angelo loti sitingalione ndi maso athu. (Yohane 4:24) Choncho, amakhala kumalo amene angelo amakhala, ndipo malo amenewo ndi osiyana kwambiri ndi dzikoli komanso kumwamba kumene timaonaku.