Mawu a M'munsi a Panapezeka zolemba zotchula dzina la wolamulira wa chigawo chinachake dzina lake Lusaniyo. (Luka 3:1) Iye analamulira chigawo cha Abilene pa nthawi yofanana ndi imene Luka anatchula.