Mawu a M'munsi
c Mfundo yakuti akufa adzauka ikhozanso kuthandiza munthu kuti apeze mtendere wamumtima. Onani nkhani yakuti “Mafunso Ochokera kwa Owerenga” mu Nsanja ya Olonda ya April 15, 2009 yomwe imafotokoza mfundo za m’Baibulo zosonyeza kuti mwina ana osabadwa amene anamwalira adzaukitsidwa.