Mawu a M'munsi
a Mwachitsanzo, Davide yemwe anali m’busa, anagwiritsa ntchito zitsanzo za zimene zimachitika ku ubusa. (Salimo 23) Mateyu, yemwe poyamba anali wokhometsa msonkho, nthawi zambiri ankatchula manambala ndiponso kuchuluka kwa ndalama. (Mateyu 17:27; 26:15; 27:3) Luka, yemwe anali dokotala, anagwiritsa ntchito mawu osonyeza kuti ankadziwa zachipatala.—Luka 4:38; 14:2; 16:20.