Mawu a M'munsi
a Ngakhale kuti anthu ena amanena kuti nkhani zina za m’Baibulo zimatsutsana, zimene amanenazo zilibe umboni. Onani Mutu 7 m’buku la Baibulo—Kodi Ndilo Mawu a Mulungu Kapena a Munthu? lofalitsidwa ndi Mboni za Yehova.