Mawu a M'munsi
b Yesu ataukitsidwa, anaonekera kwa “abale oposa 500.” (1 Akorinto 15:6) Popeza kuti pa nthawiyi otsatira ake ambiri anali ku Galileya, n’kutheka kuti imeneyi ndi nthawi yomwe yatchulidwa pa Mateyu 28:16-20. Choncho payenera kuti panali anthu ambiri pamene Yesu ankapereka lamulo loti otsatira akewo aziphunzitsa anthu kuti akhale ophunzira ake.