Mawu a M'munsi
a Pa tsiku limeneli, anthu analavulira Yesu kawiri konse. Koyamba, atsogoleri a chipembedzo ndi amene anamulavulira ndipo kachiwiri, asilikali achiroma. (Mateyu 26:59-68; 27:27-30) Ngakhale kuti Yesu ananyozedwa mwanjira imeneyi, anapirira mosanyinyirika ngakhale pang’ono. Anachita zonsezi pokwaniritsa ulosi wakuti: “Sindinabise nkhope yanga kuti asaichitire zinthu zochititsa manyazi komanso kuti asailavulire.”—Yesaya 50:6.